31 Popeza linali Tsiku Lokonzekera,+ Ayudawo sanafune kuti mitembo ikhalebe+ pamitengo yozunzikirapo tsiku la Sabata, (pakuti Sabata la tsiku limeneli linali lalikulu,)+ choncho anapempha Pilato kuti opachikidwawo awathyole miyendo ndi kutsitsa mitemboyo.