Mateyu 27:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Tsiku lotsatira, pambuyo pa Tsiku Lokonzekera,+ ansembe aakulu ndi Afarisi anasonkhana pamaso pa Pilato, Yohane 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ili linali tsiku lokonzekera+ pasika, ndipo nthawi inali cha m’ma 12 koloko masana.* Pamenepo iye anauza Ayudawo kuti: “Taonani! Mfumu yanu imeneyi!”
62 Tsiku lotsatira, pambuyo pa Tsiku Lokonzekera,+ ansembe aakulu ndi Afarisi anasonkhana pamaso pa Pilato,
14 Ili linali tsiku lokonzekera+ pasika, ndipo nthawi inali cha m’ma 12 koloko masana.* Pamenepo iye anauza Ayudawo kuti: “Taonani! Mfumu yanu imeneyi!”