Mateyu 27:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Atafika pamalo otchedwa Gologota,+ kutanthauza kuti, Malo a Chibade, Maliko 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho anafika naye kumalo otchedwa Gologota. Liwuli akalimasulira, limatanthauza Malo a Chibade.+
22 Choncho anafika naye kumalo otchedwa Gologota. Liwuli akalimasulira, limatanthauza Malo a Chibade.+