Mateyu 27:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Atafika pamalo otchedwa Gologota,+ kutanthauza kuti, Malo a Chibade, Luka 23:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Tsopano atafika pamalo otchedwa Chibade,+ anamupachika pamenepo pamodzi ndi amuna ochita zoipawo. Mmodzi anamupachika kudzanja lake lamanja, wina kumanzere kwake.+ Yohane 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo iye ananyamula yekha mtengo wozunzikirapo*+ ndi kutuluka+ kupita kumalo otchedwa Chibade, koma pa Chiheberi otchedwa, Gologota.+ Aheberi 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zinalinso chimodzimodzi ndi Yesu. Kuti ayeretse+ anthu ndi magazi ake,+ anakavutikira kunja kwa chipata.+
33 Tsopano atafika pamalo otchedwa Chibade,+ anamupachika pamenepo pamodzi ndi amuna ochita zoipawo. Mmodzi anamupachika kudzanja lake lamanja, wina kumanzere kwake.+
17 Ndipo iye ananyamula yekha mtengo wozunzikirapo*+ ndi kutuluka+ kupita kumalo otchedwa Chibade, koma pa Chiheberi otchedwa, Gologota.+
12 Zinalinso chimodzimodzi ndi Yesu. Kuti ayeretse+ anthu ndi magazi ake,+ anakavutikira kunja kwa chipata.+