Mateyu 21:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho anamugwira ndi kum’tulutsa m’munda wa mpesawo n’kumupha.+ Yohane 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo iye ananyamula yekha mtengo wozunzikirapo*+ ndi kutuluka+ kupita kumalo otchedwa Chibade, koma pa Chiheberi otchedwa, Gologota.+
17 Ndipo iye ananyamula yekha mtengo wozunzikirapo*+ ndi kutuluka+ kupita kumalo otchedwa Chibade, koma pa Chiheberi otchedwa, Gologota.+