Mateyu 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti iye anadziwa kuti anamupereka chifukwa cha kaduka.+ Maliko 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho anamugwira n’kumupha,+ ndipo anamuponya kunja kwa munda wa mpesawo.+ Machitidwe 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Munthu ameneyu, monga woperekedwa mwa kufuna kwa Mulungu ndi kudziwiratu kwake zam’tsogolo,+ ndi amene inu munamukhomerera pamtengo ndi kumupha kudzera mwa anthu osamvera malamulo.+ Machitidwe 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chotero munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa, ndipo ife ndife mboni za choonadi chimenechi.+ Aheberi 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zinalinso chimodzimodzi ndi Yesu. Kuti ayeretse+ anthu ndi magazi ake,+ anakavutikira kunja kwa chipata.+
23 Munthu ameneyu, monga woperekedwa mwa kufuna kwa Mulungu ndi kudziwiratu kwake zam’tsogolo,+ ndi amene inu munamukhomerera pamtengo ndi kumupha kudzera mwa anthu osamvera malamulo.+
15 Chotero munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa, ndipo ife ndife mboni za choonadi chimenechi.+
12 Zinalinso chimodzimodzi ndi Yesu. Kuti ayeretse+ anthu ndi magazi ake,+ anakavutikira kunja kwa chipata.+