Mateyu 21:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho anamugwira ndi kum’tulutsa m’munda wa mpesawo n’kumupha.+ Luka 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Atatero anamutulutsa+ m’munda wa mpesawo ndi kumupha.+ Pamenepa, kodi mwini munda wa mpesa uja adzachita chiyani kwa alimiwo?+ Aheberi 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zinalinso chimodzimodzi ndi Yesu. Kuti ayeretse+ anthu ndi magazi ake,+ anakavutikira kunja kwa chipata.+
15 Atatero anamutulutsa+ m’munda wa mpesawo ndi kumupha.+ Pamenepa, kodi mwini munda wa mpesa uja adzachita chiyani kwa alimiwo?+
12 Zinalinso chimodzimodzi ndi Yesu. Kuti ayeretse+ anthu ndi magazi ake,+ anakavutikira kunja kwa chipata.+