Genesis 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo Abulahamu anatenga nkhuni zokawotchera nsembe zija n’kumusenzetsa Isaki mwana wake.+ Iye ananyamula moto ndi mpeni wophera nyama, ndipo iwo anapitira limodzi.+ Mateyu 27:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pamene anali kupita, anakumana ndi Simoni, nzika ya ku Kurene.+ Iwo anasenzetsa munthu ameneyu mtengo wozunzikirapo* wa Yesu.
6 Pamenepo Abulahamu anatenga nkhuni zokawotchera nsembe zija n’kumusenzetsa Isaki mwana wake.+ Iye ananyamula moto ndi mpeni wophera nyama, ndipo iwo anapitira limodzi.+
32 Pamene anali kupita, anakumana ndi Simoni, nzika ya ku Kurene.+ Iwo anasenzetsa munthu ameneyu mtengo wozunzikirapo* wa Yesu.