Maliko 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Komanso, iwo anasenzetsa mtengo wake wozunzikirapo* munthu wongodutsa, dzina lake Simoni wa ku Kurene, amene anali kuchokera kudera la kumidzi, bambo wa Alekizanda ndi Rufu.+ Luka 23:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamene anali kupita naye, iwo anagwira Simoni, nzika ya ku Kurene, amene anali kuchokera kudera lakumidzi. Iwo anamusenzetsa mtengo wozunzikirapo,* kuti aunyamule ndi kumatsatira pambuyo pa Yesu.+ Yohane 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo iye ananyamula yekha mtengo wozunzikirapo*+ ndi kutuluka+ kupita kumalo otchedwa Chibade, koma pa Chiheberi otchedwa, Gologota.+
21 Komanso, iwo anasenzetsa mtengo wake wozunzikirapo* munthu wongodutsa, dzina lake Simoni wa ku Kurene, amene anali kuchokera kudera la kumidzi, bambo wa Alekizanda ndi Rufu.+
26 Pamene anali kupita naye, iwo anagwira Simoni, nzika ya ku Kurene, amene anali kuchokera kudera lakumidzi. Iwo anamusenzetsa mtengo wozunzikirapo,* kuti aunyamule ndi kumatsatira pambuyo pa Yesu.+
17 Ndipo iye ananyamula yekha mtengo wozunzikirapo*+ ndi kutuluka+ kupita kumalo otchedwa Chibade, koma pa Chiheberi otchedwa, Gologota.+