Mateyu 27:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pamene anali kupita, anakumana ndi Simoni, nzika ya ku Kurene.+ Iwo anasenzetsa munthu ameneyu mtengo wozunzikirapo* wa Yesu. Luka 23:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamene anali kupita naye, iwo anagwira Simoni, nzika ya ku Kurene, amene anali kuchokera kudera lakumidzi. Iwo anamusenzetsa mtengo wozunzikirapo,* kuti aunyamule ndi kumatsatira pambuyo pa Yesu.+
32 Pamene anali kupita, anakumana ndi Simoni, nzika ya ku Kurene.+ Iwo anasenzetsa munthu ameneyu mtengo wozunzikirapo* wa Yesu.
26 Pamene anali kupita naye, iwo anagwira Simoni, nzika ya ku Kurene, amene anali kuchokera kudera lakumidzi. Iwo anamusenzetsa mtengo wozunzikirapo,* kuti aunyamule ndi kumatsatira pambuyo pa Yesu.+