Miyambo 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kuopa anthu n’kumene kumatchera msampha,+ koma wokhulupirira Yehova adzatetezedwa.+ Yohane 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma panalibe amene anali kulankhula poyera za iye chifukwa choopa Ayuda.+ Yohane 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Makolo akewo ananena zimenezi chifukwa anali kuopa+ atsogoleri achipembedzo achiyuda. Pakuti iwo anali atagwirizana kale kuti, ngati wina angavomereze kuti Yesu alidi Khristu, adzamuchotsa musunagoge.+
22 Makolo akewo ananena zimenezi chifukwa anali kuopa+ atsogoleri achipembedzo achiyuda. Pakuti iwo anali atagwirizana kale kuti, ngati wina angavomereze kuti Yesu alidi Khristu, adzamuchotsa musunagoge.+