Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 9:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Makolo akewo ananena zimenezi chifukwa anali kuopa+ atsogoleri achipembedzo achiyuda. Pakuti iwo anali atagwirizana kale kuti, ngati wina angavomereze kuti Yesu alidi Khristu, adzamuchotsa musunagoge.+

  • Yohane 12:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Komabe ambiri, ngakhalenso olamulira anamukhulupirira,+ koma chifukwa cha Afarisi sanavomereze poyera, poopa kuti angawachotse musunagoge.+

  • Yohane 19:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Tsopano zitatha izi, Yosefe wa ku Arimateya, amene anali wophunzira wa Yesu koma wamseri chifukwa anali kuopa Ayuda,+ anapempha Pilato kuti amulole kuti akachotse mtembo wa Yesu, ndipo Pilato anamupatsa chilolezo.+ Choncho anafika ndi kuchotsa mtembowo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena