Mateyu 27:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 anapita kwa Pilato kukapempha mtembo wa Yesu.+ Pilato analamula kuti amupatse mtembowo.+ Maliko 15:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Yosefe wa ku Arimateya, munthu wodziwika wa m’Bungwe Lalikulu la Ayuda, amenenso anali kuyembekezera ufumu wa Mulungu,+ anapita kwa Pilato molimba mtima kukapempha mtembo+ wa Yesu. Luka 23:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Tsopano panali mwamuna wina dzina lake Yosefe, amene anali wa m’Khoti Lalikulu la Ayuda, munthu wabwino ndi wolungama.+
43 Yosefe wa ku Arimateya, munthu wodziwika wa m’Bungwe Lalikulu la Ayuda, amenenso anali kuyembekezera ufumu wa Mulungu,+ anapita kwa Pilato molimba mtima kukapempha mtembo+ wa Yesu.
50 Tsopano panali mwamuna wina dzina lake Yosefe, amene anali wa m’Khoti Lalikulu la Ayuda, munthu wabwino ndi wolungama.+