Yohane 12:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Komabe panali anthu ena amene anamukhulupirira, ngakhalenso olamulira ambiri.+ Koma sanavomereze poyera, chifukwa ankaopa kuti Afarisi angawachotse musunagoge.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:42 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 242-243 Nsanja ya Olonda,12/1/1989, ptsa. 8-9
42 Komabe panali anthu ena amene anamukhulupirira, ngakhalenso olamulira ambiri.+ Koma sanavomereze poyera, chifukwa ankaopa kuti Afarisi angawachotse musunagoge.+