Yohane 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mlonda wa pakhomo+ amamutsegulira ameneyu, ndipo nkhosa+ zimamvera mawu ake. Nkhosa zakezo amazitchula mayina ndi kuzitsogolera kutuluka nazo.
3 Mlonda wa pakhomo+ amamutsegulira ameneyu, ndipo nkhosa+ zimamvera mawu ake. Nkhosa zakezo amazitchula mayina ndi kuzitsogolera kutuluka nazo.