Yohane 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mmodzi wa ophunzira ake amene Yesu anali kumukonda,+ anakhala patsogolo pa Yesu, pachifuwa chake. Yohane 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho Yesu, poona mayi akewo ndi wophunzira amene anali kumukonda+ uja ataima chapafupi, anauza mayi akewo kuti: “Mayi, kuyambira lero, uyu akhala mwana wanu.” Yohane 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo iye anathamanga ndi kukafika kwa Simoni Petulo ndi kwa wophunzira wina,+ amene Yesu anali kumukonda kwambiri uja. Iye anawauza kuti: “Ambuye awachotsa m’manda achikumbutso+ aja, ndipo sitikudziwa kumene awaika.”
26 Choncho Yesu, poona mayi akewo ndi wophunzira amene anali kumukonda+ uja ataima chapafupi, anauza mayi akewo kuti: “Mayi, kuyambira lero, uyu akhala mwana wanu.”
2 Pamenepo iye anathamanga ndi kukafika kwa Simoni Petulo ndi kwa wophunzira wina,+ amene Yesu anali kumukonda kwambiri uja. Iye anawauza kuti: “Ambuye awachotsa m’manda achikumbutso+ aja, ndipo sitikudziwa kumene awaika.”