Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 13:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mmodzi wa ophunzira ake amene Yesu anali kumukonda,+ anakhala patsogolo pa Yesu, pachifuwa chake.

  • Yohane 21:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Zitatero, wophunzira amene Yesu anali kumukonda kwambiri uja+ anauza Petulo+ kuti: “Ndi Ambuye!” Pamenepo Simoni Petulo atamva kuti ndi Ambuye, anavala malaya ake ovala pamwamba, pakuti anali maliseche,* ndipo analumphira m’nyanja.

  • Yohane 21:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Petulo atatembenuka, anaona wophunzira amene Yesu anali kumukonda+ akuwalondola. Wophunzira ameneyu ndi amene pa chakudya chamadzulo chija anatsamira pachifuwa cha Yesu ndi kumufunsa kuti: “Ambuye, ndani amene akufuna kukuperekani?”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena