Luka 24:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Tsopano atakhala pansi n’kumadya nawo chakudya, anatenga mkate ndipo anaudalitsa, kuunyemanyema ndi kuwagawira.+
30 Tsopano atakhala pansi n’kumadya nawo chakudya, anatenga mkate ndipo anaudalitsa, kuunyemanyema ndi kuwagawira.+