Yohane 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yesu anawauza kuti: “Bwerani mudzadye chakudya cham’mawa.”+ Panalibe ngakhale mmodzi mwa ophunzirawo amene analimba mtima kumufunsa kuti: “Ndinu ndani?” chifukwa anali kudziwa kuti ndi Ambuye.
12 Yesu anawauza kuti: “Bwerani mudzadye chakudya cham’mawa.”+ Panalibe ngakhale mmodzi mwa ophunzirawo amene analimba mtima kumufunsa kuti: “Ndinu ndani?” chifukwa anali kudziwa kuti ndi Ambuye.