Yohane 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mlonda wa pakhomo+ amamutsegulira ameneyu, ndipo nkhosa+ zimamvera mawu ake. Nkhosa zakezo amazitchula mayina ndi kuzitsogolera kutuluka nazo. Yohane 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Ndili ndi nkhosa zina+ zimene sizili za khola ili,+ zimenezonso ndiyenera kuzibweretsa. Zidzamva mawu anga,+ ndipo zidzakhala gulu limodzi ndi m’busa mmodzi.+
3 Mlonda wa pakhomo+ amamutsegulira ameneyu, ndipo nkhosa+ zimamvera mawu ake. Nkhosa zakezo amazitchula mayina ndi kuzitsogolera kutuluka nazo.
16 “Ndili ndi nkhosa zina+ zimene sizili za khola ili,+ zimenezonso ndiyenera kuzibweretsa. Zidzamva mawu anga,+ ndipo zidzakhala gulu limodzi ndi m’busa mmodzi.+