Yohane 3:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Zimene iye waziona ndi kuzimva, akuchitira umboni zimenezo,+ koma palibe munthu amene akulandira umboni wake.+ 1 Akorinto 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma munthu wokonda zinthu za m’dziko* salandira zinthu za mzimu wa Mulungu, chifukwa amaziona ngati zopusa ndipo sangathe kuzidziwa,+ chifukwa zimafuna kuzifufuza mwauzimu.
32 Zimene iye waziona ndi kuzimva, akuchitira umboni zimenezo,+ koma palibe munthu amene akulandira umboni wake.+
14 Koma munthu wokonda zinthu za m’dziko* salandira zinthu za mzimu wa Mulungu, chifukwa amaziona ngati zopusa ndipo sangathe kuzidziwa,+ chifukwa zimafuna kuzifufuza mwauzimu.