Yohane 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye anavomereza osakana ayi. Anavomereza ndithu, kuti: “Ine sindine Khristu ayi.”+ Machitidwe 13:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma pamene Yohane anali kukwaniritsa utumiki wake, anali kunena kuti, ‘Kodi mukuganiza kuti ine ndine ndani? Amene inu mukumuganizira si ine ayi. Koma wina akubwera pambuyo panga, amene ine sindili woyenera kumumasula nsapato kumapazi kwake.’+
25 Koma pamene Yohane anali kukwaniritsa utumiki wake, anali kunena kuti, ‘Kodi mukuganiza kuti ine ndine ndani? Amene inu mukumuganizira si ine ayi. Koma wina akubwera pambuyo panga, amene ine sindili woyenera kumumasula nsapato kumapazi kwake.’+