Machitidwe 13:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ndipotu Yehova anatiikira lamulo lakuti, ‘Ndakuikani monga kuwala kwa anthu a mitundu ina,+ kuti mukhale chipulumutso mpaka kumalekezero a dziko lapansi.’”+
47 Ndipotu Yehova anatiikira lamulo lakuti, ‘Ndakuikani monga kuwala kwa anthu a mitundu ina,+ kuti mukhale chipulumutso mpaka kumalekezero a dziko lapansi.’”+