Yohane 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano pamene anali mu Yerusalemu pa chikondwerero+ cha pasika, anthu ambiri anakhulupirira m’dzina lake,+ ataona zizindikiro zimene anali kuchita.+
23 Tsopano pamene anali mu Yerusalemu pa chikondwerero+ cha pasika, anthu ambiri anakhulupirira m’dzina lake,+ ataona zizindikiro zimene anali kuchita.+