Yohane 4:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Choncho pamene anafika ku Galileya, Agalileyawo anamulandira, chifukwa anali ataona zonse zimene anachita pa chikondwerero ku Yerusalemu,+ pakuti nawonso anapita ku chikondwereroko.+
45 Choncho pamene anafika ku Galileya, Agalileyawo anamulandira, chifukwa anali ataona zonse zimene anachita pa chikondwerero ku Yerusalemu,+ pakuti nawonso anapita ku chikondwereroko.+