Mateyu 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Yesu anauza kapitawo wa asilikaliyo kuti: “Pita. Malinga ndi chikhulupiriro chako, chimene ukufuna chichitike.”+ Mu ola lomwelo, wantchito uja anachira. Maliko 7:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yesu atamva mawuwo anauza mayiyo kuti: “Chifukwa wanena zimenezi, pita, chiwandacho chatuluka mwa mwana wakoyo.”+
13 Kenako Yesu anauza kapitawo wa asilikaliyo kuti: “Pita. Malinga ndi chikhulupiriro chako, chimene ukufuna chichitike.”+ Mu ola lomwelo, wantchito uja anachira.
29 Yesu atamva mawuwo anauza mayiyo kuti: “Chifukwa wanena zimenezi, pita, chiwandacho chatuluka mwa mwana wakoyo.”+