Mateyu 9:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kenako anawagwira m’maso,+ n’kunena kuti: “Malinga ndi chikhulupiriro chanu zichitike momwemo kwa inu,” Mateyu 15:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo Yesu anamuyankha kuti: “Mayi iwe, chikhulupiriro chako ndi chachikulu. Zimene ukufuna zichitike kwa iwe.” Ndipo kuchokera mu ola limenelo mwana wake anachira.+ Maliko 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yesu anafunsa bamboyo kuti: “Mukuti, ‘Ngati mungathe’? Chilichonsetu n’chotheka kwa aliyense ngati iyeyo ali ndi chikhulupiriro.”+ Luka 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma amene anatumidwa aja atabwerera kunyumba, anapeza kapolo uja ali bwinobwino.+
29 Kenako anawagwira m’maso,+ n’kunena kuti: “Malinga ndi chikhulupiriro chanu zichitike momwemo kwa inu,”
28 Pamenepo Yesu anamuyankha kuti: “Mayi iwe, chikhulupiriro chako ndi chachikulu. Zimene ukufuna zichitike kwa iwe.” Ndipo kuchokera mu ola limenelo mwana wake anachira.+
23 Yesu anafunsa bamboyo kuti: “Mukuti, ‘Ngati mungathe’? Chilichonsetu n’chotheka kwa aliyense ngati iyeyo ali ndi chikhulupiriro.”+