Maliko 6:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma iye anawayankha kuti: “Inuyo muwapatse chakudya.” Pamenepo iwo anafunsa Yesu kuti: “Kodi tipite kukagula mitanda ya mkate ya ndalama zokwana madinari 200 ndi kuipereka kwa anthuwa kuti adye?”+
37 Koma iye anawayankha kuti: “Inuyo muwapatse chakudya.” Pamenepo iwo anafunsa Yesu kuti: “Kodi tipite kukagula mitanda ya mkate ya ndalama zokwana madinari 200 ndi kuipereka kwa anthuwa kuti adye?”+