Luka 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yohane anawayankha onsewo kuti: “Inetu ndikukubatizani m’madzi. Koma wina wamphamvu kuposa ine akubwera, amene ine sindili woyenera kumasula zingwe za nsapato zake.+ Iyeyu adzakubatizani ndi mzimu woyera ndi moto.+ Yohane 8:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Yesu anati: “Ndithudi ndikukuuzani, Abulahamu asanakhaleko, ine n’kuti ndilipo kale.”+ Akolose 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiponso, iye ali patsogolo pa zinthu zina zonse,+ ndipo zinthu zina zonse zinakhalapo kudzera mwa iye.+
16 Yohane anawayankha onsewo kuti: “Inetu ndikukubatizani m’madzi. Koma wina wamphamvu kuposa ine akubwera, amene ine sindili woyenera kumasula zingwe za nsapato zake.+ Iyeyu adzakubatizani ndi mzimu woyera ndi moto.+
17 Ndiponso, iye ali patsogolo pa zinthu zina zonse,+ ndipo zinthu zina zonse zinakhalapo kudzera mwa iye.+