Mateyu 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako mwamsanga, Yesu analimbikitsa ophunzira ake kuti akwere ngalawa ndi kutsogola kupita kutsidya lina, pamene iye anali kuuza anthuwo kuti azipita kwawo.+ Maliko 6:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Madzulo mdima utagwa, ngalawa ija inali pakati pa nyanja, koma iye anali yekha kumtunda.+
22 Kenako mwamsanga, Yesu analimbikitsa ophunzira ake kuti akwere ngalawa ndi kutsogola kupita kutsidya lina, pamene iye anali kuuza anthuwo kuti azipita kwawo.+