Mateyu 14:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pa nthawiyi n’kuti ngalawa ija itapita kutali pakati pa madzi, ndipo inali kukankhidwa mwamphamvu ndi mafunde+ chifukwa anali kulimbana ndi mphepo yamphamvu. Yohane 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chakumadzulo ndithu, ophunzira ake anapita kunyanja.+
24 Pa nthawiyi n’kuti ngalawa ija itapita kutali pakati pa madzi, ndipo inali kukankhidwa mwamphamvu ndi mafunde+ chifukwa anali kulimbana ndi mphepo yamphamvu.