Yohane 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Yesu anatenga mitanda ya mkate ija. Atayamika, anaigawira kwa anthu onse amene anakhala pansi aja. Chimodzimodzinso ndi tinsomba tija, anatigawira kwa anthuwo mmene aliyense anafunira.+
11 Ndiyeno Yesu anatenga mitanda ya mkate ija. Atayamika, anaigawira kwa anthu onse amene anakhala pansi aja. Chimodzimodzinso ndi tinsomba tija, anatigawira kwa anthuwo mmene aliyense anafunira.+