Mateyu 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wodala amene sapeza chokhumudwitsa mwa ine.”+ Yohane 6:66 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Pa chifukwa chimenechi ophunzira ake ambiri anamusiya ndi kubwerera ku zinthu zakumbuyo,+ ndipo sanayendenso naye.+
66 Pa chifukwa chimenechi ophunzira ake ambiri anamusiya ndi kubwerera ku zinthu zakumbuyo,+ ndipo sanayendenso naye.+