Mateyu 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yesu, podziwa zimene iwo anali kuganiza,+ ananena kuti: “N’chifukwa chiyani mukuganiza zinthu zoipa m’mitima mwanu?+ Yohane 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Yesu sanawakhulupirire+ kwenikweni chifukwa onsewo anali kuwadziwa. Yohane 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye anadziwa ndithu za munthu amene wakonza zomupereka.+ N’chifukwa chake ananena kuti: “Sikuti nonsenu ndinu oyera ayi.”
4 Koma Yesu, podziwa zimene iwo anali kuganiza,+ ananena kuti: “N’chifukwa chiyani mukuganiza zinthu zoipa m’mitima mwanu?+
11 Iye anadziwa ndithu za munthu amene wakonza zomupereka.+ N’chifukwa chake ananena kuti: “Sikuti nonsenu ndinu oyera ayi.”