Luka 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye anamuuza kuti: “Munthu iwe, ndani anandiika ine kukhala woweruza+ kapena wogawa chuma chanu?” Yohane 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti Mulungu anatumiza Mwana wake m’dziko, osati kuti mwanayo adzaweruze+ dziko, koma kuti mwa iye, dziko lipulumutsidwe.+
17 Pakuti Mulungu anatumiza Mwana wake m’dziko, osati kuti mwanayo adzaweruze+ dziko, koma kuti mwa iye, dziko lipulumutsidwe.+