Yohane 7:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Chotero Ayudawo anayamba kufunsana kuti: “Ameneyu akufuna kupita kuti, kumene ife sitingathe kukam’peza? Kapena akufuna kupita kwa Ayuda omwazikana+ mwa Agiriki ndi kukaphunzitsa Agirikiwo?
35 Chotero Ayudawo anayamba kufunsana kuti: “Ameneyu akufuna kupita kuti, kumene ife sitingathe kukam’peza? Kapena akufuna kupita kwa Ayuda omwazikana+ mwa Agiriki ndi kukaphunzitsa Agirikiwo?