Yesaya 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye adzakwezera chizindikiro mitundu ya anthu n’kusonkhanitsa Aisiraeli omwe anamwazikana.+ Ndipo adzasonkhanitsa pamodzi Ayuda omwe anabalalika, kuchokera kumalekezero anayi a dziko lapansi.+ Machitidwe 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kutangoda,+ abale anatulutsa Paulo ndi Sila ndi kuwatumiza ku Bereya. Iwo atafika kumeneko, analowa m’sunagoge wa Ayuda. 1 Petulo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Petulo mtumwi+ wa Yesu Khristu, ndikulembera inu osankhidwa ndi Mulungu,+ amene muli alendo osakhalitsa,+ amene mwamwazikana+ ku Ponto, Galatiya, Kapadokiya,+ Asia, ndi ku Bituniya.
12 Iye adzakwezera chizindikiro mitundu ya anthu n’kusonkhanitsa Aisiraeli omwe anamwazikana.+ Ndipo adzasonkhanitsa pamodzi Ayuda omwe anabalalika, kuchokera kumalekezero anayi a dziko lapansi.+
10 Kutangoda,+ abale anatulutsa Paulo ndi Sila ndi kuwatumiza ku Bereya. Iwo atafika kumeneko, analowa m’sunagoge wa Ayuda.
1 Ine Petulo mtumwi+ wa Yesu Khristu, ndikulembera inu osankhidwa ndi Mulungu,+ amene muli alendo osakhalitsa,+ amene mwamwazikana+ ku Ponto, Galatiya, Kapadokiya,+ Asia, ndi ku Bituniya.