Yohane 5:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Sindikufuna ulemerero wochokera kwa anthu,+ Yohane 13:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mulungunso payekha amulemekeza iye,+ ndipo amulemekeza nthawi yomwe ino. Machitidwe 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza+ Mtumiki+ wake Yesu, amene inu munamupereka+ ndi kumukana pamaso pa Pilato, Pilatoyo akufuna kumumasula.+
13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza+ Mtumiki+ wake Yesu, amene inu munamupereka+ ndi kumukana pamaso pa Pilato, Pilatoyo akufuna kumumasula.+