Yohane 7:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chotero pamene anali kuphunzitsa m’kachisimo Yesu anafuula kuti: “Inu mukundidziwa ine komanso mukudziwa kumene ndikuchokera.+ Ndipo ine sindinabwere mwa kufuna kwanga,+ alipo ndithu amene anandituma,+ koma inu simukumudziwa.+
28 Chotero pamene anali kuphunzitsa m’kachisimo Yesu anafuula kuti: “Inu mukundidziwa ine komanso mukudziwa kumene ndikuchokera.+ Ndipo ine sindinabwere mwa kufuna kwanga,+ alipo ndithu amene anandituma,+ koma inu simukumudziwa.+