Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 12:51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 Kodi mukuganiza kuti ndinabweretsa mtendere padziko lapansi? Ayi ndithu, koma ndinabwera kudzagawanitsa anthu.+

  • Yohane 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndipo panali manong’onong’o ambiri onena za iye m’khamu lonse la anthulo.+ Ena anali kunena kuti: “Amene uja ndi munthu wabwino.” Ndipo ena anali kunena kuti: “Ayi si munthu wabwino amene uja, iye akusocheretsa anthu ambiri.”

  • Yohane 9:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ena mwa Afarisiwo anayamba kunena kuti: “Munthu ameneyu si wochokera kwa Mulungu, chifukwa sasunga Sabata.”+ Ena anayamba kunena kuti: “Koma munthu wochimwa angachite bwanji zizindikiro+ zoterezi?” Choncho panakhala kugawanika+ pakati pawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena