Mika 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti mwana wamwamuna akunyoza bambo ake. Mwana wamkazi akuukira mayi ake+ ndipo mkazi wokwatiwa akuukira apongozi ake aakazi.+ Adani ake a munthu ndi anthu a m’banja lake.+ Mateyu 10:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Musaganize kuti ndinabweretsa mtendere padziko lapansi, sindinabweretse mtendere+ koma lupanga. Yohane 7:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Choncho khamu la anthulo linagawanika pa nkhani ya iye.+ Yohane 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ena mwa Afarisiwo anayamba kunena kuti: “Munthu ameneyu si wochokera kwa Mulungu, chifukwa sasunga Sabata.”+ Ena anayamba kunena kuti: “Koma munthu wochimwa angachite bwanji zizindikiro+ zoterezi?” Choncho panakhala kugawanika+ pakati pawo.
6 Pakuti mwana wamwamuna akunyoza bambo ake. Mwana wamkazi akuukira mayi ake+ ndipo mkazi wokwatiwa akuukira apongozi ake aakazi.+ Adani ake a munthu ndi anthu a m’banja lake.+
16 Ena mwa Afarisiwo anayamba kunena kuti: “Munthu ameneyu si wochokera kwa Mulungu, chifukwa sasunga Sabata.”+ Ena anayamba kunena kuti: “Koma munthu wochimwa angachite bwanji zizindikiro+ zoterezi?” Choncho panakhala kugawanika+ pakati pawo.