Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 41:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Koma munthu amene ndinali kukhala naye mwamtendere, amene ndinali kumukhulupirira,+

      Munthu amene anali kudya chakudya changa,+ wakweza chidendene chake kundiukira.+

  • Yeremiya 12:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Abale ako komanso anthu a m’nyumba ya bambo ako akuchitira chinyengo,+ ndipo mofuula akukunenera zinthu zoipa ali kumbuyo kwako. Usawakhulupirire m’pang’ono pomwe, ngakhale kuti akukuuza mawu abwino.+

  • Mateyu 10:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Kunena zoona, adani a munthu adzakhala a m’banja lake lenileni.

  • Yohane 13:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Sindikunena nonsenu, ndikudziwa amene ndawasankha.+ Koma zili choncho kuti Malemba akwaniritsidwe,+ paja amati, ‘Munthu amene anali kudya chakudya changa wanyamula chidendene chake kundiukira.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena