Miyambo 30:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pali m’badwo umene umatemberera ngakhale abambo awo ndiponso umene sudalitsa ngakhale amayi awo.+ Ezekieli 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu anyoza abambo ndi amayi awo mwa iwe.+ Mlendo wokhala mwa iwe amuchitira zinthu mwachinyengo.+ Azunza mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye.”’”+ Mateyu 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Komanso munthu adzapereka m’bale+ wake ku imfa, ndipo bambo adzapereka mwana wake. Ana adzaukira makolo awo ndipo adzawaphetsa.+ Luka 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso makolo anu enieniwo,+ abale anu, anthu oyandikana nanu ndi mabwenzi anu, adzakuperekani, ndipo adzapha ena a inu.+
7 Anthu anyoza abambo ndi amayi awo mwa iwe.+ Mlendo wokhala mwa iwe amuchitira zinthu mwachinyengo.+ Azunza mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye.”’”+
21 Komanso munthu adzapereka m’bale+ wake ku imfa, ndipo bambo adzapereka mwana wake. Ana adzaukira makolo awo ndipo adzawaphetsa.+
16 Komanso makolo anu enieniwo,+ abale anu, anthu oyandikana nanu ndi mabwenzi anu, adzakuperekani, ndipo adzapha ena a inu.+