Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 82:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Chitirani chilungamo anthu onyozeka ndi ana amasiye.*+

      Chitirani chilungamo anthu osautsika ndi osauka.+

  • Salimo 94:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Amapha mkazi wamasiye ndi mlendo wokhala m’dziko lawo,+

      Ndipo amaphanso ana amasiye.*+

  • Yesaya 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Phunzirani kuchita zabwino.+ Funafunani chilungamo.+ Dzudzulani munthu wopondereza ena.+ Weruzani mwachilungamo mwana wamasiye.*+ Thandizani mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+

  • Yeremiya 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 ngati simudzapondereza mlendo wokhala pakati panu, mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye,+ komanso ngati simudzakhetsa magazi a munthu wopanda mlandu m’dziko lino,+ ndiponso ngati simudzatsatira milungu ina, zimene zingakubweretsereni tsoka,+

  • Zekariya 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Musamabere mwachinyengo mkazi wamasiye,+ mwana wamasiye,*+ mlendo+ kapena munthu wosautsika.+ Musamakonzerane chiwembu mumtima mwanu.’+

  • Malaki 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Anthu inu ndidzakuyandikirani kuti ndikuweruzeni.+ Sindidzazengereza kupereka umboni+ wotsutsa amatsenga,+ achigololo,+ olumbira monama+ komanso ochita chinyengo pa malipiro a munthu waganyu.+ Sindidzazengereza kupereka umboni wotsutsa anthu ochitira chinyengo mkazi wamasiye,+ mwana wamasiye*+ ndiponso opondereza alendo.+ Anthu amenewa sakundiopa,”+ watero Yehova wa makamu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena