Yesaya 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Akalonga ako ndi aliuma ndipo ndi anzawo a mbala.+ Aliyense wa iwo amakonda ziphuphu+ ndipo amafunafuna mphatso.+ Mwana wamasiye samuweruza mwachilungamo ndipo ngakhale mlandu wa mkazi wamasiye safuna kuuweruza.+ Yesaya 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo amachita zimenezi n’cholinga choti asamvetsere mlandu wa anthu onyozeka ndiponso kuti anthu anga osautsika awalande chilungamo.+ Amateronso kuti atenge akazi amasiye ngati katundu wolanda ndiponso kuti atenge ana amasiye.*+
23 Akalonga ako ndi aliuma ndipo ndi anzawo a mbala.+ Aliyense wa iwo amakonda ziphuphu+ ndipo amafunafuna mphatso.+ Mwana wamasiye samuweruza mwachilungamo ndipo ngakhale mlandu wa mkazi wamasiye safuna kuuweruza.+
2 Iwo amachita zimenezi n’cholinga choti asamvetsere mlandu wa anthu onyozeka ndiponso kuti anthu anga osautsika awalande chilungamo.+ Amateronso kuti atenge akazi amasiye ngati katundu wolanda ndiponso kuti atenge ana amasiye.*+