Yesaya 29:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 amene amachimwitsa munthu ndi mawu ake,+ amene amatchera msampha munthu wodzudzula ena pachipata,+ ndiponso amene amagwiritsira ntchito mfundo zopanda umboni pokankhira pambali munthu wolungama.+ Maliro 3:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndi kupotoza chiweruzo cha munthu pa mlandu wake, Yehova savomereza zimenezi.+ Amosi 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo akufunitsitsa kuti fumbi la padziko lapansi ligwere pamitu ya anthu wamba+ ndipo sakuchitira chilungamo anthu ofatsa.+ Mwana pamodzi ndi bambo ake akugona ndi mtsikana mmodzi+ ndi cholinga chofuna kuipitsa dzina langa loyera.+
21 amene amachimwitsa munthu ndi mawu ake,+ amene amatchera msampha munthu wodzudzula ena pachipata,+ ndiponso amene amagwiritsira ntchito mfundo zopanda umboni pokankhira pambali munthu wolungama.+
7 Iwo akufunitsitsa kuti fumbi la padziko lapansi ligwere pamitu ya anthu wamba+ ndipo sakuchitira chilungamo anthu ofatsa.+ Mwana pamodzi ndi bambo ake akugona ndi mtsikana mmodzi+ ndi cholinga chofuna kuipitsa dzina langa loyera.+