Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 10:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iwo amachita zimenezi n’cholinga choti asamvetsere mlandu wa anthu onyozeka ndiponso kuti anthu anga osautsika awalande chilungamo.+ Amateronso kuti atenge akazi amasiye ngati katundu wolanda ndiponso kuti atenge ana amasiye.*+

  • Amosi 5:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pakuti ndadziwa kuchuluka kwa zochita zanu zondipandukira+ ndiponso kukula kwa machimo anu,+ inu amene mukuchitira nkhanza munthu wolungama,+ amene mukulandira ndalama za chitsekapakamwa+ ndiponso amene mukupondereza anthu osauka+ pachipata cha mzinda.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena