Ekisodo 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Musachitire nkhanza mlendo wokhala pakati panu kapena kum’pondereza,+ chifukwa anthu inu munalinso alendo m’dziko la Iguputo.+ Miyambo 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Usabere munthu wonyozeka chifukwa chakuti ndi wonyozeka,+ ndipo usapondereze wosautsika pachipata cha mzinda.+
21 “Musachitire nkhanza mlendo wokhala pakati panu kapena kum’pondereza,+ chifukwa anthu inu munalinso alendo m’dziko la Iguputo.+
22 Usabere munthu wonyozeka chifukwa chakuti ndi wonyozeka,+ ndipo usapondereze wosautsika pachipata cha mzinda.+