Mateyu 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Yesu anamuyankha kuti: “Nkhandwe zili ndi mapanga ndipo mbalame zam’mlengalenga zili ndi zisa, koma Mwana wa munthu alibiretu poti n’kutsamira mutu wake.”+ 2 Akorinto 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti mukudziwa kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti ngakhale kuti iye anali wolemera, anakhala wosauka chifukwa cha inu,+ kuti inuyo mulemere+ kudzera m’kusauka kwake.
20 Koma Yesu anamuyankha kuti: “Nkhandwe zili ndi mapanga ndipo mbalame zam’mlengalenga zili ndi zisa, koma Mwana wa munthu alibiretu poti n’kutsamira mutu wake.”+
9 Pakuti mukudziwa kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti ngakhale kuti iye anali wolemera, anakhala wosauka chifukwa cha inu,+ kuti inuyo mulemere+ kudzera m’kusauka kwake.