2 Akorinto 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa mukudziwa kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti ngakhale kuti anali wolemera, anakhala wosauka chifukwa cha inu,+ kuti inuyo mulemere kudzera mʼkusauka kwakeko. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:9 Nsanja ya Olonda,2/15/1992, ptsa. 16-171/15/1992, ptsa. 16-17
9 Chifukwa mukudziwa kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti ngakhale kuti anali wolemera, anakhala wosauka chifukwa cha inu,+ kuti inuyo mulemere kudzera mʼkusauka kwakeko.